Top Latest News & Reports

Boma kudzera ku Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi (DoDMA) mogwirizana ndi mabungwe osiyanasiyana likupereka thandizo la chakudya kwa anthu 5.7 miliyoni okhudzidwa ndi njala pansi pa ndondomeko ya 2024-25 Lean Season Response. Ntchitoyi idayamba…
…Ofesi Ya Kazembe wa Dziko la China Lapereka Matumba a Ufa 1,320 Kwa Maanja Okhudzidwa ndi Njala Ofesi ya Kazembe wa Dziko la China kuno ku Malawi Lachinayi (pa 7 November, 2024) lapereka matumba a…
Having successfully held a forum on Climate Disaster Risk Financing (CDRFI) and Insurance in Blantyre from 29th to 31st October, delegates drawn from 24 African countries visited Mulanje District where they interacted with communities and…
…Boma La India Lapereka Matumba 22,000 a Mpunga; Othandizira Okhudzidwa ndi Njala Boma la India lapereka ma tani 1,100 (omwe ndi matumba 22,000 olemera makilogilamu 50 lililonse) a mpunga ku Boma la Malawi kuti athandizire…

Visitors Counter

1003308
Today
Yesterday
This Week
Last Week
This Month
Last Month
All days
489
1903
2916
1000392
10002
47999
1003308

Your IP: 3.145.12.136
2024-12-21 12:12