Top Latest News & Reports

NTCHITO YOKHAZIKITSA NDONDOMEKO YOPEREKA THANDIZO LA CHAKUDYA KU MAANJA OKHUDZIDWA NDI NJALA KU CHIKWAWA NDI MWANZA
01 Oct 2024

NTCHITO YOKHAZIKITSA NDONDOMEKO YOPEREKA THANDIZO LA CHAKUDYA KU MAANJA OKHUDZIDWA NDI NJALA KU CHIKWAWA NDI MWANZA

Boma kudzera ku Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi Loweruka (pa 21 September) yakhazikitsa ntchito yopereka thandizo ku maanja okhudzidwa ndi njala m'boma la Chikwawa. Nduna Yoona za Madzi ndi Ukhondo a Abida Mia ndi omwe anatsogolera mwambowu womwe unachitikira m'dera la Mfumu Yaikulu Kasisi.

M'boma la Mwanza, mwambo ngati womwewu unachitikira Lachisanu (pa 20 September) kwa Mfumu Yaikulu Nthache motsogozedwa ndi Wachiwiri kwa Nduna Yoona za Maboma Aang'ono a Owen Chomanika.

Visitors Counter

861402
Today
Yesterday
This Week
Last Week
This Month
Last Month
All days
3149
5301
29193
801570
52238
83139
861402

Your IP: 3.237.15.145
2024-10-11 21:39