Top Latest News & Reports

Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa Dziko Lino Dr. Michael Usi anakayendera  ntchito yopereka thandizo kwa maanja okhudzidwa ndi njala m'maboma a Chikwawa ndi Thyolo.
13 Jan 2025

Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa Dziko Lino Dr. Michael Usi anakayendera ntchito yopereka thandizo kwa maanja okhudzidwa ndi njala m'maboma a Chikwawa ndi Thyolo.

Akuluakuluwa saadalekere pompo koma kukhotanso ku Kampu ya Nyamithuthu, yomwe ikusunga maanja pafupifupi 2,000 omwe adathawa zipolowe m’dziko la Mozambique. Uku anacheza ndi anthu akuluakulu komanso ana (omwe anawapeza akusewera mpira ndi masewero osiyanasiyana), kumva za mmene akukhalira komanso mavuto omwe akukumana nawo.

Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa Dziko Lino Dr. Michael Usi Lachisanu (pa 27 December) anakayendera ntchito yopereka thandizo kwa maanja okhudzidwa ndi njala m'maboma a Chikwawa ndi Thyolo.

Pa ulendowu, a Usi anayankhulana ndi ena mwa okhudzidwa za mmene ntchitoyi ikuyendera.

Iwo anathandizanso kunyamulira matumba a chimanga anthu okhudzidwa, kuphatikizapo achikulire.

Visitors Counter

1074526
Today
Yesterday
This Week
Last Week
This Month
Last Month
All days
104
1038
2299
1063805
21819
36664
1074526

Your IP: 18.97.14.91
2025-02-18 02:43